CHARITY SHOP
Ndine Takuya, ndipo ndine mtsogoreli wa tigwirane madja (shake hands) ndakhara ndikuyenda mayiko.ndayenda mayiko oposa one hundred ngati tourist.ndipo nawona zithu zambiri zopasa chidwi za chirengedwe ndi Anthu.ndipo ndiri ndi chikumbitima cha zinthu zimene ndinawona mumaulendo anga onse 100. Zikomo.
Mumaulendo angawa ndinawona Anthu ambiri ombvutika ndi umphawi.
Ndiganiza ma tourisit ambiri amayenda ndi ndalama zochepa kuphatikizaso ine.chocho sititha kukwanisa kuthandiza Anthu ombvutika akatipepha
.Ndinawona ndi kumbva chisoni ndi Anthu osawuka. Nditamariza ulendo wanga kubwerera ku japan ndinafika bwino. Koma tsiku ndi tsiku ndikamakhara. Utsiku ndi usana ndimaganizirebe za Anthu osauka ndinawawona, Akulu ndi Ana. Ndipo malingariro awiri kuchokera pansi pa mtima wanga amandipeza.lingarilo loyamba: kuyenda mayiko adziko lapasi. lingarilo lachiwiri: kuthandiza Ana osawuka amene ndinakumana nawo angakhare ndiri tourist.
Mwamwayi muthawiyi ndinakumana ndi ma tourisit azanga ku Tsubane Nligata amene amagwira ntchito Zawo morimbika ndi mozipereka. Modzi mwa iwo ndi mwini wake wa TRIANGL GUEST HOUSE. Anandifusa ngati ndiri ndi chidwi choyesa kuthandiza nawo Ana osauka .
Ndipo ndinasakha kuyambisa tigwirane madja(shake hands). Chifukwa ndimakhurupirira kuti Anthu timatha kukumana ndikusiyana
Dziko lonse lapansi.
Most SHAKE HANDS members experience traveling around the world and discovering the world. The group's activity is based on these backpackers.
Let me explain a bit more. These people travel to many parts of the world with their own backpackers. Because they like to travel freely and without extra supplies.
All goods in the SHAKE HANDS market are bought and purchased by these people from around the world.
The trend in the SHAKE HANDS market is different from other stores that offer similar products.
We travel as a traveler to most parts of the world and buy whatever is lovely and symbolic of that country.
We also travel to deprived and unusual areas so that we can buy unique products in that area.
The SHAKE HANDS group plans to deliver products around the world directly to the real customers by using the experience of various travels and crafts from localities around the world. It also inspires customers to buy from a point in the world.
Due to numerous trips by the group, this group has enough information about real poverty in the world, and therefore the problem of global poverty is never hidden from us, which is why we buy the products that are provided by the needy, and never buy products with high sales. In this way, we can make the profit from this market accessible to the children of the unprotected or poorly supervised people who we met around the world.
The SHAKE HANDS band is trying to create a joyful cycle that members of that group are.
We also all share this joy with all the people or needy people who we bought from them, and the customers of this marketplace, as well as the children we need to help them.
The SHAKE HANDS band are working in this field and we will strive to develop this group and share this joy and sense of friendship.
Yamazaki Takuya
MoreLeader
Yusuke Hasegawa
MoreMusician
Click for listening music
Ryutaro
Moreインド🇮🇳で1人旅を経験し、現地で暮らしている人々の生活や文化、価値観に興味を持ち、青年海外協力隊でバングラデシュ🇧🇩・フィジー🇫🇯に行き、現地の人と共に生活をする。 その後、中南米を放浪。
日本に戻り、人に元気を与えられるようなゲストハウスを始めようと物件探してをしていたところ、パラグライの宿で出会ったTakuyaさんから連絡があり、SHAKE HANDSの構想について聞かせてもらった。
今後は人々の交流の場となるBARを作り、ゲストハウスも併設する予定。人と人が繋がれる環境をつくり、仲間の輪を広げ、喜怒哀楽を分かち合い、助け合い、共に成長して行きたい